DISPLAY Buku la M'Baibulo Genesis Ekisodo Levitiko Numeri Deuteronomo Yoswa Oweruza Rute 1 Samueli 2 Samueli 1 Mafumu 2 Mafumu 1 Mbiri 2 Mbiri Ezara Nehemiya Esitere Yobu Masalimo Miyambo Mlaliki Nyimbo ya Solomo Yesaya Yeremiya Maliro Ezekieli Danieli Hoseya Yoweli Amosi Obadiya Yona Mika Nahumu Habakuku Zefaniya Hagai Zekariya Malaki Mateyu Maliko Luka Yohane Machitidwe Aroma 1 Akorinto 2 Akorinto Agalatiya Aefeso Afilipi Akolose 1 Atesalonika 2 Atesalonika 1 Timoteyo 2 Timoteyo Tito Filimoni Aheberi Yakobo 1 Petulo 2 Petulo 1 Yohane 2 Yohane 3 Yohane Yuda Chivumbulutso Chaputala 1 2 3 4 Buku la Malaki Machaputala 1 2 3 4 Mitu 1 Yehova amakonda anthu ake (1-5) Ansembe ankapereka nsembe zosalongosoka (6-14) Dzina la Mulungu lidzakhala lalikulu pakati pa anthu a mitundu ina (11) 2 Ansembe ankalephera kulangiza anthu (1-9) Ansembe ankayenera kuphunzitsa anthu za Mulungu (7) Anthu ankathetsa mabanja pa zifukwa zosamveka (10-17) “‘Ndimadana ndi zoti anthu azithetsa mabanja,’ watero Yehova” (16) 3 Ambuye woona anabwera kudzayeretsa kachisi (1-5) Mthenga wa pangano (1) Anawalimbikitsa kuti abwerere kwa Yehova (6-12) Yehova sasintha (6) “Bwererani kwa ine ndipo ine ndidzabwerera kwa inu” (7) ‘Bweretsani chakhumi chonse ndipo Yehova adzakudalitsani’ (10) Anthu olungama ndiponso anthu oipa (13-18) Buku la chikumbutso linalembedwa pamaso pa Mulungu (16) Kusiyana pakati pa wolungama ndi woipa (18) 4 Eliya adzabwera tsiku la Yehova lisanafike (1-6) ‘Dzuwa la chilungamo lidzawala’ (2) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Malaki—Zimene Zili Mʼbukuli BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA (LOKONZEDWANSO MU3 2023) Malaki—Zimene Zili Mʼbukuli Chichewa Malaki—Zimene Zili Mʼbukuli https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg nwt Malachi p. 1642