NSANJA YA OLONDA Na. 3 2020 | Mulungu Wachikondi Adzatipatsa Madalitso Osatha
Werengani kuti mudziwe madalitsowa, chifukwa chake mungawakhulupirire komanso mmene mungawapezere.
Mungasangalale ndi Madalitso Osatha Ochokera kwa Mulungu Wachikondi
Kodi mumalakalaka kukhala m’dziko lopanda nkhondo, chiwawa komanso matenda? Zimenezi si maloto chabe koma ndi malonjezo ochokera kwa Mulungu.
Mlengi Wathu Wachikondi Amatisamalira
Mulungu amasamalira banja lake ngati mmene bambo wachikondi angachitire. Kodi amachita bwanji zimenezi?
Kodi Mlengi Wathu Amatithandiza Bwanji Kudziwa Malonjezo Ake?
Kodi Mulungu anagwiritsa ntchito bwanji aneneri kuti alembe uthenga wake?
Kodi Mawu a Mulungu Anasinthidwa?
Werengani kuti mudziwe zimene akatswiri anapeza zokhudza Baibulo limene tili nalo masiku ano.
Timaphunzira za Mulungu Kuchokera kwa Aneneri Ake
Aneneri okhulupirika atatu amatithandiza kuphunzira za Mulungu komanso zimene tingachite kuti tidzalandire madalitso.
Muzipemphera Kuti Mulungu Akudalitseni
Kodi tingapemphere bwanji kuti Mulungu azimva mapemphero athu komanso kutidalitsa?
Anthu Amene Amamvera Mulungu Amalandira Madalitso
Werengani kuti mudziwe njira ziwiri zimene Mulungu amatidalitsira tikamamumvera.
Kodi Tingasonyeze Bwanji Kuti Timakonda Anzathu?
Nthawi zina kusonyeza ena chikondi si kophweka komabe tikhoza kukwanitsa.
Anthu Amene Amathandiza Ena Amalandira Madalitso
Kodi Mulungu adzatidalitsa bwanji tikamayesetsa kuthandiza anthu?
Mukhoza Kusangalala ndi Madalitso Ochokera kwa Mlengi Wathu Mpaka Kalekale
Kodi moyo padzikoli udzakhala wotani Mulungu akadzakwaniritsa zimene analonjeza Abulahamu?
Kodi Munayamba Mwadzifunsapo Kuti:
Werengani kuti mupeze mayankho a mafunso okhudza Mulungu komanso mavuto athu.