NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) June 2024
M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira August 12–September 8, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 23
Yehova Akutiitana Kuti Tikhale Alendo Ake
Idzaphunziridwa mlungu wa August 12-18, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 24
Pitirizani Kukhala Alendo a Yehova Mpaka Kalekale
Idzaphunziridwa mlungu woyambira August 19-25, 2024.
MBIRI YA MOYO WANGA
Yehova Wakhala Akuyankha Mapemphero Anga
Kodi n’chiyani chomwe chinatsimikizira Marcel Gillet yemwe anali wachikulire kuti Yehova ndi “Wakumva pemphero”?
Mafunso Ochokera kwa Owerenga
Kodi mawu akuti “Mudzawayang’anira” opezeka pa Salimo 12:7, akunena za “ovutika” (vesi 5) kapena “mawu a Yehova” (vesi 6)?
NKHANI YOPHUNZIRA 25
Muzikumbukira Yehova Yemwe ndi “Mulungu Wamoyo”
Idzaphunziridwa mlungu wa August 26–September 1, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 26
Muzidalira Yehova Yemwe ndi Thanthwe Lanu
Idzaphunziridwa mlungu wa September 2-8, 2024.