Mboni za Yehova Padziko Lonse

Anguilla

Mfundo Zachidule—Anguilla

  • 15,000—Chiwerengero cha anthu
  • 62—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 1—Mipingo
  • Pa anthu 273 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

A Mboni Akugwira Mwakhama Ntchito Yothandiza Anthu Omwe Anakhudzidwa Ndi Mphepo Zamkuntho

Maofesi a Nthambi a Mboni za Yehova akufotokoza zimene akuchita pothandiza komanso kutonthoza mwauzimu anthu okhudzidwa ndi mphepo yamkuntho ya Irma ndi Maria.