Mfundo Zachidule—Guyana
- 798,000—Chiwerengero cha anthu
- 3,280—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 46—Mipingo
- Pa anthu 249 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
ZOCHITIKA PA MOYO
Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Guyana
Kodi tingaphunzire zotani kwa anthu amene anatumikirapo kumene kukufunika olalikira ambiri? Kodi zimene iwo ananena zingakuthandizeni bwanji kukonzekera kukatumikira kudziko lina ngati mukufuna kutero?