Zatsopano pa JW.ORG
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Zoti Ndiphunzire—Kukhala Olimba Mtima Ena Akamatitsutsa
Kodi tingaphunzire chiyani pa kulimba mtima kwa Yeremiya ndi Ebedi-meleki?
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Funso Losavuta Limene Aliyense Angathe Kufunsa
Mofanana ndi Mary, mungathe kuyambitsa maphunziro a Baibulo angapo pongofunsa funso losavuta.
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Zimene Tingachite Kuti Tikhale Bwenzi Lenileni
Baibulo limanena kuti anzathu enieni amatithandiza pakagwa mavuto.
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Muzipewa Mzimu Wodzikonda
Anthu ambiri m’dzikoli amaona kuti ndi ofunika kupatsidwa ulemu wapadera, ufulu komanso kuchitiridwa zinthu m’njira yapadera. Onani mfundo za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni kupewa maganizo amenewa.
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
“Sindinakhalepo Ndekhandekha”
Onani chifukwa chake Angelito Balboa amakhulupirira kuti nthawi zonse Yehova ankakhala naye, ngakhale pamene akukumana ndi mayesero ovuta.
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
February 2025
M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira April 14–May 4, 2025.
NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU
March–April 2025
NKHANI
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 7 la 2024
Mulipotili, timva zokhudza abale ndi alongo athu padziko lonse komanso tionera mbali yocheza ndi abale atsopano a m’Bungwe Lolamulira, omwe ndi M’bale Jody Jedele ndiponso Jacob Rumph.
NKHANI
“Yehova Adzandifupa”
NKHANI
Zokhudza Misonkhano ya Mayiko: A Mboni Anatulutsa Baibulo pa Bwalo la Masewera a Mpira wa Padziko Lonse ku Seoul
A Mboni za Yehova anatulutsa Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika pa Msonkhano wa Mayiko wa mutu wakuti, “Pitirizani Kufunafuna Ufumu wa Mulungu Choyamba.”