Davide Anayembekezela Yehova
Onani cinathandiza Davide kuyembekezela Yehova kuti adzakonze zopanda cilungamo zimene zinali kumucitikila. Malinga na 1 Samueli 24:2-15; 25:1-35; 26:2-12; Salimo 37:1-7.
Mungakondenso Izi
MAPHUNZILO AMENE TINGATENGEMO M’BAIBO
Davide na Sauli
N’cifukwa ciani mmodzi wa anthu awa amazonda mnzake? Nanga mnzakeyo acita zinthu motani?