Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

NSANJA YA MLONDA Na. 6 2017 | Ni Mphatso Iti Yoposa Zonse?

MUGANIZA BWANJI?

Kodi wopambana onse pa kupeleka mphatso n’ndani?

“Mphatso iliyonse yabwino ndi yangwilo imacokela kumwamba, pakuti imatsika kucokela kwa Atate wa zounikila zonse zakuthambo, ndipo iye sasintha ngati kusuntha kwa mthunzi.”Yakobo 1:17.

Magaziniyi ya Nsanja ya Mlonda idzatithandiza kudziŵa mphatso imodzi yoposa zonse, yocokela kwa Mulungu.

 

NKHANI YA PACIKUTO

“Inali Mphatso Yabwino Koposa Imene Sin’nalandilepo”

Kodi mungakonde kupeleka kapena kulandila mphatso yabwino kwambili?

NKHANI YA PACIKUTO

Kusakila Mphatso Yabwino Koposa

Kupeza mphatso imene munthu angakonde kwambili si cinthu copepuka. Ndipo kuti mphatso ioneke kuti ni yamtengo wapatali zimadalila woilandila.

NKHANI YA PACIKUTO

Ni Mphatso Iti Yoposa Zonse?

Pa mphatso zonse zimene Mulungu watipatsa, pali mphatso imodzi yoposa zonse.

Kodi Yesu Anali Kuoneka Bwanji Kweni-kweni?

Kwa zaka zambili Yesu wakhala akuonekela m’mapikica a anthu ambili ojambula zithunzi. Kodi Baibo imafotokoza zotani zokhudza mmene iye anali kuonekela?

Kuona Zolakwa Moyenelela

Kaya tili na zaka zingati, kapena luso labwanji, tonse timalakwitsa. Nanga tingacite ciani tikalakwitsa?

N’cifukwa Ciani​—Pali ma Baibo Osiyana-siyana?

Kudziŵa ciyambi cake kudzakuthandizani kumvetsa cifukwa cake pali zimasulilo za Baibo zosiyana-siyana.

Kodi Akhristu Ayenela Kukondwelela Khrisimasi?

Kodi ophunzila a Yesu anali kukondwelela Khrisimasi?

Kodi Baibo Imakamba Ciani?

Liu lakuti Aramagedo limacititsa mantha. Kodi limatanthauza ciani kweni-kweni?

Madanga Ena Opezeka pa Intaneti

N’cifukwa Ciani Mboni za Yehova Sizikondwelela Khrisimasi?

Anthu ambili amakondwelela Khrisimasi ngakhale kuti amadziŵa ciyambi cake. Dziŵani cifukwa cake Mboni za Yehova sizikondwelela Khrisimasi.