NSANJA YA MLONDA November 2015 | Kodi Mboni za Yehova Ndani?

Kuti mupeze yankho, pitani kumene mungapeze cidziŵitso coculuka.

NKHANI YA PACIKUTO

Kodi Mboni za Yehova Ndani?

Kodi mfundo zimene zili m’nkhani ino zikufanana ndi maganizo anu?

NKHANI YA PACIKUTO

Kodi Mboni za Yehova Ndi Anthu Otani?

Timapezeka kulikonse.

NKHANI YA PACIKUTO

Kodi Mboni za Yehova Zimakhulupilila Ciani?

Kukhulupilila Baibulo kumatithandiza kukhala ndi cikhulupililo.

NKHANI YA PACIKUTO

Kodi Ndalama Zoyendetsela Nchito Yathu Timazipeza Bwanji?

Kodi ndalama zimacokela kuti? Nanga zimagwilitsidwa nchito bwanji?

NKHANI YA PACIKUTO

N’cifukwa Ciani Timalalikila?

Tili ndi zifukwa zazikulu zitatu zimene timalalikilila padziko lonse

NKHANI YA PACIKUTO

N’cifukwa Ciani Anthu Amapemphela?

Anthu amapemphela pa zifukwa zosiyanasiyana.

NKHANI YA PACIKUTO

Kodi Pali Wina Amene Akumvetsela?

Kuti Mulungu amve pemphelo lathu, tifunika kucita zinthu ziŵili zofunika kwambili.

NKHANI YA PACIKUTO

N’cifukwa Ciani Mulungu Amatilimbikitsa Kupemphela?

Palibe njila ina imene timalandilila madalitso kuposa kupemphela kwa Mulungu.

NKHANI YA PACIKUTO

Pemphelo—Kodi Lingakuthandizeni Bwanji?

Tingapindule bwanji ngati timapemphela tsiku ndi tsiku?

Kodi Munakhumudwa ndi Mulungu?

Kodi munadzifunsapo kuti, ‘N’cifukwa ciani Mulungu walola kuti zimenezi zindicitikile?’

Kuyankha Mafunso a m’Baibulo

Ndani angathetse umphawi?

Madanga Ena Opezeka pa Intaneti

Kodi Nkhondo ya Aramagedo N’ciyani?

Mawu akuti Aramagedo amapezeka kamodzi kokha m’Baibo. Koma nkhondo imene mawuwa amatanthauza imachulidwa m’Baibo lonse.